Mwadzuka bwanji?
Tithokonze nonse munatenga nawo gawo.Ndakatulo zolembedwa bwino kwambiri.Koma omwe ndakatulo zawo zapeza ma likes wochuluka ndi awa:
Elijah Chisale 43
Astrepa Bright 37
Kandiero Tunguza 35
Mahajir Umali 19
Aubrey Sally Chikwate 16
Amenewa tiwajambula ndakatulo zimene atipatsazi ndipo tiwathandizira kutumiza ndakatulo zimenezi mma radio
Amene maina Ali apo yakhulani ndi Amfumu Kenneth Khondiwa pa 0997465040
Poetry Association of Malawi
PAM brings together persons involved in the promotion of poetry in the country; to preserve Malawian culture through poetry; and edu-entertain the public.
Poetry Association of Malawi (PAM) was founded in 1997 when a group of poets met at Kamuzu Stadium upper ground among whom were Mr. Laurent Namarakha, late Aubrey Nazombe, Edward Chitseko and late George Chiingeni. PAM was registered on 4th September, 1998 by the Registrar General under the Trustees Incorporation Act of 1962. The Poetry Association of Malawi has the responsibility of ensuring the
Mwaswera bwanji?
Tisaname masakhidwa avuta anthu tachuluka.Pali magawo awiri, ena muli pa Facebook komanso pa page pano, ndipo ena Sali piano mwinanso alive foni kapena Ali NDI ya keypad.
Ndiye taonjezera tijambula anthu 10.Asanu omwe muli pano, asanu omwe palibe.
Kusakha kwa pano kukhala motere, aliyense alembe ndakatulo yake yomwe ikufuna kujambulidwa ndipo yomwe ikhale NDI ma likes ambiri yawina.
Mulemba text.
Malire Sunday 6pm
Big shout out to my new rising fans! Mada Kanama, Shaib Shaffie, Elijah Chisale
Mwadzuka bwanji?
Ndi mlakatuli uti kwanuko amene mumadziwa kuti ndi dolo koma akuchepekedwa kulowa studio?
Timupatse danga loti ajambule ndakatulo imodzi ku Amfumu Media Production.
Atchuleni tisakha 5 woyambilira
NB. Only audios
31/05/2026
`NAFENSO TIZILIRA - The wait is over. The poem is out now.
Stream it on YouTube. Link below 👇
NAFENSO TIDZILIRA ( A POEM ON MENTAL HEALTH) A poem by Chifundo Vuso Jere ft Gideon Palm Tree, Patwel Phiri and Enea Kachigamba.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Contact the school
Telephone
Website
Address
Blantyre