Kodi athu aboma akaparamura timagova kuti khani yawo iri kukhothi sitidavepo m'mene miranduyawo imathera ?komaso kodi akapexeka orakwa ndende yake m'makawaikakuti ?nagabwaji atorakhani sapiriza mwatsatanetsatane zamirandu ya athu oterewakuiurutsa ? Zimagotherakuti akuimbibwa murandu mapeto amuranduwo sikawirikawiri kutiuza m'mene zathera kutizathabwaji ? Wapezeka orakwa amujaja zaka zigati kapena osarakwa chinachitika ndichani?: Muzitidziwitsa chonde chifukwa mukaiyambakhani yaathu andare kapena otchuka kuti apezeka ndi murandu mukaiwurutsa khanija timavetsera ndichidwi koma imagoti zi!! Zimakhara bwaji???
Kuyakhurapo zadziko
TaKurandirani nose
Mwadzukabwaji amarawari
Nwadzuka bwaJi abare ndi arigo
Kuno kumalawi kod azitsogoreri Ana anu chimene xaphuzirira komkuno ndi chani ? Please mutandiya kodtiganene kuti school zathuzi mumatipatsa kumudzikunozi pachirugamo chake kuyambira 1-8 -form :1-4:chitozake ndiurondatu bas ndikunama?
14/07/2022
Pamene dziko ramarawirino riripamavuto adzaoneni ndipamene azitsogoreri akagarika kumanena kutizikuyenda chabwino poti mmidzimu simupitamo athuamidzimu tikukharagati ziweto Moyo ovetsa chisoni ogoyembekeza ifa pamene Malawi momuno ena or Jara saidziwa anaawo
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Telephone
Website
Address
Lilongwe
YOHANE