Autice Mdzuma the poet

Autice Mdzuma the poet

Share

Poet and Chinese student

03/05/2026

mdalitso wina ukukusemphano chifukwa cha aja mudawakwiira aja, tawakhululukiran muone chikondi cha mulungu lero

Happy Sunday🥳

02/05/2026

nanga momwe wavutira Malawi basi wina azidulitsa phon nanga munda🤣

02/05/2026

kutengeka, kufuna kufanana level ndi a nebor zotsaitira zake ndi zimenezo 🤣🤣

02/05/2026

Album yomwe Mlakatuli Raphael Sitima akutulutsa mawa, only Autice mdzuma the poet featured one of his poem . tiyeni tikumane ku lilongwe CCAP hall mawa laliwisili tikayapatse motsooo🥳🥳🥳🥳

01/05/2026

Nthawi ya moyo zochitika ndizambiri.
ngati wakuswani mtima ndiye kuti muli mu nthawi ya moyo. open new chapter 😎

01/05/2026

The staaaaaaaageeee master Raphael sitima ali ndi show kuseli kwa mawa uku, kulalikira walalikira koma tsiku ili ndilomaliza, tiyeeeeenni tonse tikakumane ku lilongwe CCAP hall kodi inu zabwino ayiiiiii???🥳🥳🥳

Photos from Autice Mdzuma the poet's post 01/05/2026

LISTEN TO MY STORY ON LABOURS DAY 🙏🙏🙏🙏🙏🙏😭😭

I was born into a poor family of eight children in a rural village, life was never easy. We could not always afford proper clothes or even a good meal, but the desire to learn never left me.

I started primary school at the age of 8, later went on to Dowa Secondary School, and by God’s grace, I passed my MSCE becoming the only person in my entire village to achieve it. That moment changed everything.

I continued my journey at Kasungu Teachers Training College, and in 2018, I began my career as a professional teacher. But I didn’t stop there.

In 2024, I took another bold step and enrolled at MUST to study a Bachelor of Arts in Languages and Communication, specializing in Chinese and English.

Looking back, I see not just struggle, but strength. Not just lack, but determination. And above all, God’s hand guiding me every step of the way.

I thank God for this journey 🙏🙏🙏

Happy labours day

30/04/2026

from inbox
"I am 30yrs man, am looking for FAIRY used woman of about 25-28 yrs"

30/04/2026

Alamu anu akuchimuna abwera ndi mwana kwanu, akukuuzani kuti musamuletse amalira. ladies let's goo🤣

30/04/2026

ena simundidzwa koma mukachita search pa Google ikupatsani information yonse, osaiwala tili ndi album launch ya Raphael sitima ku lilongwe pa 3 May. lets cast our last tickets now.

29/04/2026

palia tickets awiri a show ya Raphael ndipereka kwa amene comment yake sikhala ndi like
tchulani ubwino umodz okhala single😂

29/04/2026

malinga mkudula kwa fuel, ku Dowa stikupanga nawo zibwana😂

Want your school to be the top-listed School/college in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address

Lilongwe