18/06/2025
Chidziwitso
Tikhala tikupereka maphunziro ntchito za manja maka luso losoka zovala, kumanga tsitsi ndi kuotchelera ku madzulo kwa Boma la Dedza motere:
Maphunziro: Tailoring, Salon and Welding
Malo: Ndebvu Village,
Tsiku Loyambira: July 7, 2025
Tsiku Lodzamaliza: October 31, 2025
Fiizi : MWK200,000 (4 months) pa phunziro
Yolembetsera: MWK20,000 pa phunziro
Worksuit/Uniform: MWK35,000
Malo ndi wolimbirana, lembetsani kuti mupeze mwayi wa maphunziro antchito za manja:
0999 80 68 70 / 0998488200
Director
15/06/2025
02/07/2024
27/11/2023
03/08/2023