29/05/2026
azathu ku Catholic University of Malawi atidzidzimutsa
K42000000
The Catholic University of Malawi
congratulations Grace Joyce Chilembwe
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from BUNDA EYE, Box 219, Bunda, Lilongwe.
BUNDA EYE is a media platform developed by Bunda Communication and Journalism students under the Department of Agricultural Education and Development Communication at LUANAR.
29/05/2026
azathu ku Catholic University of Malawi atidzidzimutsa
K42000000
The Catholic University of Malawi
congratulations Grace Joyce Chilembwe
29/05/2026
ACHINYAMATA NDI ATSOGOLERI AMAWA~BINGU
Bungwe la Eagles Institute lomwe limagwira ntchito m'magawo osiyanasiyana makamaka gawo lolimbikitsa maufulu a anthu, kupereka upangiri kwa achinyamata omwe akusaka ntchito, achinyamata womwe akuwonjezera maphunziro awo komanso zamaphunziro lagawa buku lero ku LUANAR pa kampasi ya Bunda.
Buku li lomwe akulitcha kuti "PEACE, LOVE & LIBERTY, likufotokoza komanso kuphunzitsa m'mene anthu angakhalire mwamtendere, mwachikondi,mwaufulu komanso kuipa kwa nkhondo pa umoyo wa anthu.
Patricia Bingu yemwe ndi Communication Officer wa bungweli anatsindika kuti bungwe lawo limaperekaso uphungu kwa achinyamata womwe ali ndi mabungwe kapena amene akufuna kuyambitsa mabungwe makamaka akasowekera upangiri opeza thandizo la ndalama.
Iwoso anawonjezera kuti mwambo ogawa buku li upitilira m'masukulu ena monga LUANAR NRC, Nalikule,Deayang ndi ena ambiri.
Mkufotokoza kwawo, a Patricia Bingu anawuzaso ophunzira apa LUANAR Bunda kampasi kuti asamaziyang'anire pansi pakuti Iwo nde atsogoleri amawa.
Kumbali ya ophunzira inayankhura ndi Felix Samson yemwe anafotokoza kuti buku li ndilofunika kwambiri pa umoyo wa ophunzira komanso achinyamata kuti azikhara ozindikira za maufulu awo, za mtendere komanso chikondi.
(Wolemba : Conscious Leonard 29/05/2026)
Photo credit:Mayamiko Mphutsi
29/05/2026
Today we are celebrating the birthday of our Senior Editor, Chimwemwe Kawonga kasonda
May your day be filled with joy, greatness and happiness
Happy birthday to you 🥳🎊🎉
29/05/2026
Bunda Eye Spotlight ✨
Congratulations to Happier Khunga on graduating with a Bachelor of Science in Environmental Sciences (Credit).
As Co-founder of Access Malawi Online, Happier has been a great partner to Bunda Eye working with us on podcast productions and collaborative media projects of youth-driven storytelling initiatives.
We celebrate your achievement and wish you continued success.
🔥My Distinction journey start 🔥
after encouraged by Mk400,000 gifts
Escom will no longer disturb me anymore
Thank you everyone for trusting us during this period, welcome our new followers your support energizes our team to improve
🙏🙏🙏
Lera,lera...
Iyi ndi Agricultural extension class of 2026 graduation
Students graduating with degree in education sciences testifying there Journey