Liwonde Trends

Liwonde Trends

Share

Trending stories in MACHINGA and Balaka

14/02/2026

Liwonde Malawi

07/02/2026

woza woza

09/01/2026

Big shout out to my new rising fans! Gizy G Shaib, ßøï Påtïzö

28/12/2025

Fun facts

0. Munthu umalota kwa 5 seconds basi koma ukamalongosola umakhala ngati walota usiku onse. Ukalota kopitilira pamenepo ndi zija mumanva kuti afera kutulo.

1. Mzimu wamunthu umalemera 0.023grams.

2. 90% ya anthu omwe amanena kuti anabadwa pa 25 December kapena 1 January amakhala akunama.

3. Mwana aliyense akamayamba m’mimba amakhala wamkazi kenako amazasintha nkhukhala wamwamuna ndi chifukwa chake amuna amabadwa ndi mabere.

3. Dzikoli likuzungulira kwambiri masiku ano kuposa kale.

4. Ndalama zapepala pompano zisiya kugwira ntchito anthu azingotumizirana. Apa mpomwe pazakhale ndalama imodzi paja koma anthu sazazindikira mwachangu.

5. Maloto omaliza kulota kumamawa kumasamala nawo amalosera zinthu zoti zichitika.

6. Ma scientists apeza earth ina mlengalenga koma sitingapiteko chifukwa kwatalika kunyamuka nde kuti ukalambira munjira olo chomwe wakweracho chitamathamanga 1 million kilometer per second.

7. Uchi ndi chakudya chokhacho chomwe sichimaola.

8. Munthu yemwe anamwalira dzaka 500 zapitazo kudzuka lero akhozanso kumwalira pompopompo chifukwa mpweya unaonongeka koma ife tauzolowera.

9. Mbayani primary ndi school yokhayo yomwe ili ndi ana ambiri Africa yonse.

10. Mwezi sumawala umangonyezimira nde dzuwa limawalira mweziwo then mweziwo mkumawala.

17/12/2025

Big shout out to my newest top fans! Andrew Banda, Shuq Dada, Ronard Cosmass

02/12/2025

Big shout out to my new rising fans! Peace Dzikatiphindu

02/12/2025

Barbershop ya bwino mu Liwonde mu ndi iti

29/10/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Thedson Nankumba, Elias Ackim, Frank Chipala, Patrick Luwis, Elisha Njala, Matiyas Siranji, Hamuza Idana, Peace Pasavute Kazembeh, Chikondi Hajih, Fosper Mw, Benzema Gibo Harrison, Leejoh Iott, Aggie Namaona, Dyson Dafutala, Dollah Jamalie, Sajid Goodson, Man Chip Kamot, Jack Wa Kalinde, Asheeby James, Pretty Díãñãh, Fwiji Fård, Mahamud Wayisoni, Amoss Akar, Chisomo M Bwana, Nafishah Beib, Shuku SG, Rich Mpire, Shabani Walusa, Ellen Beib, Khenge Butao, Scott Kasupe, Cynthia Mumba, Darren Doreen, Baba Masamu, Marrium Med, Brian Bagga, Anaff Julius

29/09/2025

kodi kwanuko chimanga chili pa bwanji

Want your school to be the top-listed School/college in Liwonde?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address

Liwonde
Liwonde