Riaz Chitukuko Official

Riaz Chitukuko Official

Share

Educator. Mentor. Explorer

25/02/2026

Mbalame ku Kazakhstan kuno mu winter zimasowa .

20/02/2026

Pemphero mphande akapanga post galimoto yake ndiye Congratulations,
Ine kupanga post yanga matama ett ? aMalawi mukhalike πŸ˜‚πŸ™ŒπŸ½

Follow me guys 🫑

19/02/2026

Iyi si mvula, ndi Snow ameneyu.
Kupangila anzathu aku Mangochi inu πŸ˜‚

18/02/2026

Mukapeza nthawi, kafiken pa Liwonde National Park .

17/02/2026

Malape Pillars ndi miyala yayitali yomwe ili m’boma la Machinga .

Mbiri, Miyambo ndi Zikhulupiriro

Kwa akuluakulu akale m’dera la Machinga, Malape Pillars ankawawona ngati:
β€’ Malo opatulika
β€’ Malo okhala mizimu
β€’ Malo amene anthu amamva mawu osawoneka kapena kuwona zinthu zachinsinsi
Choncho achinyamata samaloledwa kupita popanda chilolezo cha akulu akulu .

Masiku ano, Malape Pillars akudziwika ngati:
β€’ Malo okopa alendo (tourist attraction)
β€’ Malo ochitira maulendo a mapiri (hiking)
β€’ Malo ofunikira pachikhalidwe ndi pa chilengedwe cha Malawi

Recommendation:
Ndizofunika kupeleka value ndikusamalira malowo kuti azithandiza pa zachuma ndi kuteteza chikhalidwe.

17/02/2026

Zochitika ku Machinga .

Apolisi ku Machinga ati akusakasaka anthu awiri omwe akuwaganizira kuti apha bambo wazaka 38, a Fred Ligomeka, atawapeza akuba nkhuku panyumba ina m'bomali.

Mneneri wa polisi ya Machinga, a Western Kansire, ati a Ligomeka usiku watha anapita kukaba nkhuku ku nyumba ya munthu wina m'mudzi mwa Lipagani.

Iwo ati mwini nyumba atazindikira kuti kwabwera wakuba anayamba kukuwa zomwe zinadzutsa khwimbi la a anthu n'kugwira oganirizidwawa nkuyamba kuwamenya.

A Kansire ati kutsatira kumenyedwaku oganiziridwawa anavula kwambiri ndipo anatengeredwa kuchipatala cha Chikwewo, komwe achipatala atsimikiza kuti afa kaamba kotaya magazi.

A Fred Ligomeka amachokera mudzi mwa Mwikawa mfumu yayikulu Ngokwe ku Machinga

(Copied)
Side note : tisiye kuba

15/02/2026

MACHINGA Malawi πŸ‡²πŸ‡Ό

15/02/2026
15/02/2026

Hello. Ine ndi Riaz waku Machinga , page iyi ndiyanyuwani ndipo izikhala ikupanga focus zochitika zambiri zaku Machinga komanso zina zosiyanasiyana. Ngat ingakupezen, pangan FOLLOW.
Be the first to follow and let’s normalize UNITY.

Want your school to be the top-listed School/college in Machinga?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Website

Address

Chikweo
Machinga
P.0 BOX 69