06/06/2026
a Head ndi zizukulu
am a Muslim
06/06/2026
a Head ndi zizukulu
03/05/2026
Chips chilipobe?
Marriage is allow in Islam and is also farila and sunna
Ndiwa sabath
11/04/2026
Family π«π¨βπ©βπ§βπ§
Pazifukwa zina kwa anthu ongolonjeza koma osaonetsa kusintha zinthu posazindikira kuti kumabwera wina oposela iweyo umagwa nawo udindo oti unali wako
in 2030 choose wisely
21/03/2026
Eid Mubarak
20/03/2026
Eid Mubarak family
Tsiku la QiyΔmah Kukavuta.
Allah akamuwuza munthu awerenge yekha buku lake, ndipo kapolo akalakatula zonse anali kuchita .
kenako Allah azati kwaiye:
βE iwe kapolo wanga, kodi angelo anga olemba ntchito (al-kiram al-katibΔ«n) anakupondeleza polemba chinachake comwe sunachite?β
Munthuyo adzayankha:
βAyi Mbuye wanga.β
Kenako Allah akati:
βKodi pali chilichonse ungakane mu zomwe ukuona (mβbuku la zintchito zako)?β
Iye adzayankha:
βAyi Mbuye wanga, palibe ndikuka.βπ
Kenako pakamwa pake padzatsekedwa, ndipo ziwalo zake monga manja, mapazi ndi khungu lake zidzayamba kulankhula kufotokoza kuchitira umboni zomwe ankachita pa dziko lapansi.
ππππππ
copy and paste
14/03/2026
ukupanga zofoila iweyoπππ