Kunenepa kusaponse apa
Chipraj Independent schools
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chipraj Independent schools, School, Mwanza, Mwanza.
Morning people
18/01/2023
04/01/2023
Akuluakulu tiyeni tithandidzane kufunafuna dzina la zipatso izi.
Zimakhala ndi tiubweya tina tobaya ndipo si zipwete, zangofanana mmaonekedwe. Mtengo wake umathanso kukhala pa nyumba ngati maluwa koma umakhala ndi mingaminga.
Mmadera ena a mdziko la Zambia, anthu amazidziwa zipatsozi ndi dzina loti " Saroti" , pamene kumaderanso ena mdziko la Mozambique, zimadziwika ndi dzina loti " Pamoti ". NANGA KWANUKO?
Koma tikufuna kungokumbutsanako za mungagwiritsire ntchito zipatsozi kuthana ndi matenda osiyanasiyana.
Timathyola zipatsozi ndi kuzipondaponda kenako nkuphatikidza ndi utomoni wa mango ( pang'ono) nkumamwa mamawa musadye kalikonse. Mukatero , basi mwathana ndi mavuto monga kupota kwa pamtima komanso kumva kuwawa pansi pamchombo munthu ukamataya madzi, maansazi , tizilonda ta pakhosi , kamwazi ndi matenda ambiri.
Kwa amene timakonda kudziwa mmene timachidzira matenda osiyanasiyana ndi za chilengedwe izi Osaiwala kupanga like page ili la Mfumu Solomo Pabwalo, tizionera limodzi zinthuzi MWAULELE.
04/01/2023
Panopa kwacha ndipo ena tili mnjira kupita ku munda, ku ntchito , ku sukulu, ndi ku malo osiyanasiyana. Komano mutakumana ndi iti pa njira kapena mmunda m***a kunena kuti mwakumana ndi tinyama tanji ?
Tingokumbutsanako kuti mmadera ena muno muMalawi tinyamati timadziwika ndi dzina loti LIKONGWE ngakhale tilipo magulumagulu. Nthawi zambiri tikakhala mmunda timagwira zilombo zosiyanasiyana zomwe zimaononga mbewu ndipo timadya mbalame, nkhanu, madzira a mbalame ndi nyama zosiyanasiyana, abuluzi , analimata ndi zina. Mmayiko ena mmalo moweta amphaka , amaweta tinyama iti.
Ayi tangoti tiwowe nawo tinyamati, KWANUKO TIMADZIWIKA NDI DZINA LANJI?
Osaiwala kupanga like page ili la Mfumu Solomo Pabwalo tizionera limodzi zinthuzi
03/01/2023
Dziko la malawi lili ndi zipani zosiyanasiyana zomwe zina sizimadziwika ngakhale pang'ono, tikuyenera kudziwapo zipani zina months Malawi Congress Party (MCP), Democratic Progressive Party (Dpp), United Transformation Movement (UTM), Mbakuwaku Movement for Development (MMD) kungonena ochepa chabe.
Malawi tikuyenera kukhala ndi cholinga chofuna kusankha chipani chimene chili ndi cholinga chofuna kutukula mtundu wa amalawi osati kungofuna kukhutitsa mimba zawo
Pamene tatsala ndi chaka chimodzi kuti tisankhenso tiyeni tidzasankhe mwa mnzeru kuti tisadzanong'oneze bondo ayi.
03/01/2023
Dziko la Malawi layamba kuoneka ngati chipalamba tsopano
Mneneri wa Catholic church in malawi wayankhula zimenezi pamene amakayendera anthu okalamba m'boma la zomba
Kunena kwawo akuti amalawi tikuyenera kusintha zochita zathu kuti chilengedwe chibwererenso mchimake.
us
2022 BEST PERFOMERS TEACHER TRAINING COLLEGE AWARD
Best Administration
-Karonga Teachers College
College of the year
-Kasungu Teachers College
Most improved TTCs
-Chiradzulu Teachers College
'Schart
CHIBWEZI MPAKA 7 YEARS
MUKUTENGA MASTERS ?
"iiiiii KOMA KUMANENA NTHAWI YABWINO ABALE," watero mkulu wa bungwe la ISAMA
Mtsogoleri wa bungwe la eni sukulu zomwe si zaboma la Independent Schools Association of Malawi ( ISAMA) Wycliffe Chimwendo wadandauala ndi ganizo lomwe komiti yapadera ya mtsogoleri wa dziko lino yoyang'anira za nthenda ya COVID 19 komanso kolera yoimitsa kutsekulira kwa sukulu mwachikhadzakhadza.
Izitu malingana ndi komitiyi, zachitika ndi cholinga chofuna kuonetsetsa kuti kufala kwa nthendayi kwachepa.
Koma mmawu ake, a Chimwendo ati komitiyi imayenera kubwera ndi chiganizochi msanga kusiyana ndi momwe zakhaliramu ndi cholinga choti nawonso akonzekere bwino.
Iwo ati mwachitsanzo iwo alandira kale ophunzira ena omwe anali atafika kale msukulu zawo kaamba koti uthengawu wabwera mochedwa.
Malingana ndi chikalata chomwe chasainidwa ndi nduna ya zaumoyo Khumbize Kandodo Chiponda chati sukulu za pulaimale ndi sekondale za mmizinda ya Blantyre ndi Lilongwe sisatsekulire kaye mawa kaamba koti mlili wa kolera wanyanya.
IndependentSchool online
Me:Sir tabwelezani apopo sum yo sinamve
Sir: English please
Me: A bas ndamvesano 😂😂
online
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Mwanza