20/02/2023
Pomwe ndimajambula nyimbo ya Zonke Too Fresh ya ndinayuza mankhwala ine ndinayuza skill yapa life skillsππ
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from WISE OLD SCHOI, School, Area 1b, Mzuzu.
20/02/2023
Pomwe ndimajambula nyimbo ya Zonke Too Fresh ya ndinayuza mankhwala ine ndinayuza skill yapa life skillsππ
thumutchuleni mzanu amene ankavina bwino chibelemuda changanga aziwe k*t mmamnyadila
Ine LAZZ G πππ
mtumbuka osamba ndi LAZZ G yekha Martse anali mtonga osamba continue resting in peace big bro mtonga osamba
Atoht Manje umafanana ndi Mafuken lkkkk
Don't trust love hahahaha ufunse Ife tikuuza zambiri π
Eya zoti amunafe ndiagalu tikuvokeleza koma inuso chemwali pezani galu wanu mmodzi osati agalu mpakana atatu,seven ndinu mlenje kodi?
Amene sanapezebe Adam kapena Eve wake mpakana pano nde k*ti iyeyo ndichinjoka chija
Madala Mutu wa Phyzo mupangidwe feature pa nyimbo ya tambwali ija ndi mutu wanuo mungakomese video ππ
Che Wikise1992 9 vs 2 ak*t ngati ulibe adam or eve nde k*t ndiwe chinjoka chuja π
Ching'aning'ani ndi MR JOKES samachapa mano anthuwaπππ pomwe CheChe Mandota - Dr J.S.ChikakudanChe Mandota - Dr J.S.ChikakudaDChe Mandota - Dr J.S.Chikakuda Che Mandota - Dr J.S.ChikakudaSChe Mandota - Dr J.S.Chikakudai handsome ndi mano omwe much love brasaπ