Zochitika Ku Phalombe in Malawi

Zochitika Ku Phalombe in Malawi

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zochitika Ku Phalombe in Malawi, College & University, Phalombe.

07/02/2025
07/02/2025

Say goodbye to ants and cockroaches with this magical leaf

07/02/2025

Izi ndi zinthu 8 zofunikila kuti mudzipanga check mukamagula phone yoti imagwila kale ntchito (second hand phones). Guys ngini iyiyi muitengere serious apo biii mudzagula phone yoti kungogwilitsa ntchito masiku awili, kupezeka yalokedwa:

1. Pangani check khalidwe la phone

Chophimba (Screen): Onani ngati chisali chobooka, chagwetsedwa, kapena chili ndi madontho.

Thupi la foni: Yang’anani ngati foni yawonongeka kapena ili ndi zipsera.

Mabatani & Mabowo: Yesani mabatani onse (Volume, Power, Home) ndi doko lotchaja kuti muwone ngati zikugwira bwino.

Kamera & Flash: Tsegulani kamera, yesani zithunzi ndi video, onaninso ngati flash ikugwira.

2. Battery & Liwiro la Foni

Battery Health: Yesani kuona ngati battery ikuchita bwino kapena imatsitsa mwachangu.

Kuyaka Mwachangu: Ikani charger kuti muone ngati foni imayaka bwino.

Liwiro la Foni: Tsegulani mapulogalamu angapo kuti muwone ngati foni siyochedwa kapena kuyesa kupanga download mapulogalamu nkuona ngati sizikuvuta.

3. Chiwonetsero & Kukhudzika (Touch Sensitivity)

Penyetsetsani chophimba chonse kuti muwone ngati palibe madera amene sakhudzika.

Sinthani kuwala (brightness) kuti muwone ngati chophimba chikugwira bwino

4. Speaker, Microphone & Vibration

Sewerani nyimbo kapena kanema kuti muwone ngati ma speaker akugwira bwino.
Record voicenote kuti muwone ngati maikolofoni ikugwira.
Yesani vibration kuti muwone ngati imagwira.

5. Ma Network & Kulumikizana

Ikani SIM card yanu kuti muwone ngati ma network akugwira.
Yesani mobile data, Wi-Fi, ndi Bluetooth.
Tsegulani Google Maps kuti muwone ngati GPS ikugwira bwino.

6. Storage & IMEI Check

Pitani kuma Settings > Storage kuti muwone ngati mphamvu yosungira ikugwirizana ndi zomwe zinalembedwa.

Dial * #06 # kuti muone IMEI number, kenako mufufuze pa IMEI.info kuti muone ngati foni sinabedwe kapena sili yokhoma (blacklisted).

7. Software & Account Locks (gawo lofunika zedi pamagawo onse)

Yang’anani ngati pali software yatsopano (updates).

Onetsetsani kuti foni ilibe Google Account (FRP lock) kapena iCloud lock (pa ma iPhone).

Fufutani zonse mu foni (Factory Reset) kenako yambitsaninso foni kuti muone ngati siyifunanso ma password amwini woyamba.

8. Zowonjezera & Chitsimikizo (Warranty)

Onani ngati pali charger, ma earphones, ndi bokosi lake (kumashop amwenye)

Funsani risiti kapena chitsimikizo (warranty) ngati chilipo. (Mashop amwenye).

Mukatsata izi simuzakhumudwa ndi phone ya second hand, ena amati ya sekeni.

Pangani follow Stargic , kuti mukhale katakwe pa technology.

01/11/2024

Mafumu onse a ku Dedza auzidwa kuti alembe anthu awo plus ID number; Akutumiza kwa nduna ina ya mphamvu kwambiri m'boma la Chakwera. Potero ndunayo ikumatumiza kwa Annabel Mtalimanja kumene mayinawo akumayikidwa mu machine a Malawi Electoral Commission.

Pa chithunzipo tikuona ena mwa mayina ochokera ku Dedza amene alowa kale mu machine a Smartmatic. Bungwe la MEC likugwira ntchito ndi MCP komanso NRB pofuna kusokoneza chisankho. Ndikunena pano, mafumu ena akupitilizabe kulemba anthu mmaboma a Salima ndi Nkhotakota. Nayenso Chakwera akukumana ndi mafumu a ku Dedza pa nkhani yomweyo.

24/10/2024

Most people don't know the power of this Underestimate Backyard Miracle Plant …. See more👀👇

24/10/2024

This plant, known as the asthma plant, can be found in almost every garden or yard, but many people are unaware of its powerful benefits… See more👀👇

Want your school to be the top-listed School/college in Phalombe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address

Phalombe