Dolo 🔥
Mulenje Entertainment
Bring Art To Life 🎙🎼🎵
Good Morning to you all
Hello , How are you wherever you are ?
05/02/2026
Katundu alipo ndthu , Woti iyayi
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rodney Kondowe, ÉÉ Vëñømh Géñå BädyÉÉ, Yamikan Charles, Mlenje Ck
26/01/2026
Inu ati chani awa? 😂 😂
26/01/2026
Cha Cha 🔥
26/01/2026
Driemo 🔥
26/01/2026
Ati chani awa ? 😂
😂 mutipwetekera ana
26/01/2026
"BUNGWE LA PAM LIKUPHA ULAKATULI"
Bungwe la Ulakatuli ku Malawi(Poetry Association of Malawi) sikuchitapo kanthu pa zodandaula zomwe alakatuli amakhala nazo.
Kwakhala kukumveka nkhani zochuluka , alakatuli kudandaula kuti atsogoleri a PAM sakukwanitsa kuthandiza ulakatuli ku Malawi kuno kupita patsogolo. Mu kafukufuku wathu , tapeza kuti kuli alakatuli ambiri omwe akhoza kunyamula Malawi pa nkhani yolemba ndi kulakatula koma zikuvuta kamba ka utsogoleri wa Robert Chiwamba.
Kutengera Zomwe walemba Mlakatuli Mercy Mbeta , zikuonesa kuti amachitidwa nkhanza posayankhidwa ndi adindowa , Mercy ndi mmodzi mwa atsikana odziwa kusakaniza mau kudzera mu ulakatuli. Mercy Mbeta anatchuka kwambiri zaka za 2019 2020 2021 2022 , koma pano kuli ziii.
Chonde ku PAM ko, ngati zanu zinayera kale sibwino kupondereza ana omwe akubwerawa.
Shout out to my newest followers! I'm excited to have you onboard! Joel Ps Mughogho, Leroy Namarika, Lywell Mwandira, Brendah Kang'ombe
Thanks so much
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Telephone
Website
Address
Balaka