AbuHafs Abdulmalik

AbuHafs Abdulmalik

Share

The page is meant to remind one another with regards to the teachings of our religion Islam

14/03/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rafiq Mtengula, Kidd Kuchawo, Uthmaan J Bamus

07/10/2023
26/06/2023

بسم الله الرحمن الرحيم
Tsiku lodikililidwa latulukila!الحمد لله

Kuchokera pamene yalowa mangrib mwaswali ija,lero ndipa 9 Dhulhijjah,tsiku la arafah,kotelo kucha kwa m'mawa(27th June)tikuyenela kusala kudya,malipilo ake nkukhululukidwa machimo a chaka chapita ndi chomwe chilinkudza, m'mene mtumiki صلي الله عليه وسلم adatiphunzisila.
Tsiku lomwe Angelo amatsika,
Limene Allah amawapulumusa anthu ambili ku kanjo ya moto,limene mtumiki akulisimba kuti Dua yake ndiyabwino kuposa matsiku ena onse,tiyeni tichulukise kupepha chinkhululuko,kupepha zabwino zomwe zili kwa Allah,Kuchulukisa kupanga Dhikr makamaka mawu oti: لا إله إلا الله وحده لا شريك له،له الملك وله الحمد وهو علي كل شيء قدير mtumiki anawachemelela mawuwa ponenakuti:ndi Dua yabwino yomwe iye komanso atumiki am'mbuyo adapanga.
قال عطاء الخراساني رحمة الله عليه:إن استطعت أن تخلو بنفسك عشية عرفة فافعلAtwa Allah amuchitile chisoni adati: ngati ungakwanise kukhala pawekha kubindikila,kumapanga mapephelo utsiku ngati uno omwe uli wa arafah,panga zimenezo.

Timpephe Allah atipase chilimbikiso komanso atiyakhe mapephelo anthu

18/06/2023

MWEDZI wa Dhulhijjah wawoneka mmawa Monday ndi 1 Dhulhijjah

16/06/2023

Ndinampepha Allah koma sanandiyakhe/sanandipase
Palibe chifukwa chosiila/kugwela ulesi kupanga Dua
Mtumiki anatiuzakuti msilam akapanga Dua yomwe ilibe ntchimo kapena kudula Ubale,chimodzi mwa zitatu chimachitika
1.Allah atha kukuyakha,nkuona zipatso
2.Atha osakuyakha koma kukuchosela vuto linalake
3.Atha osakuyakha koma kukakupasa zabwino tsiku la chiweluzo,munthu nkukadabwakuti zachokela kuti!
Allah a

16/06/2023

Zabwela mu Hadeeth yosimikizika kuti tsiku ngati lero la Jumuah,muli hour imene nsilamu akakumana nayo akumpepha Allah zabwino,amapasidwa,ngakhale kuti tikuyenela kuchulukisa kupanga ma Dua tsikuli,mu hour iliyonseyo,komabe pali chiembekezo chachikulu kuti ndi hour yomwe ilipakati pa asir ndi mangrib,kotelo tiyeni tichilukise ma Dua
Allah atilandile

23/03/2023

Tizidya Dakwi tisasemphane ndizabwino

Want your school to be the top-listed School/college in Domasi?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Domasi