19/05/2026
Pali ndalama apa. Tiyeni nazo!
Private Technical Colleges Association of Malawi-PRITECAM
M.I.R.A.C.L.E is a Technical Institute where M.I.R.A.C.L.E stands for Marianist Institute of Rural Artisans for Christian Life Education.
It was Established in 1999 in Karonga District by Marianist Brothers of the Roman Catholic Church.
19/05/2026
Pali ndalama apa. Tiyeni nazo!
Private Technical Colleges Association of Malawi-PRITECAM
Koda Ida.
Osanamizira kuti sitinawerenge uthenga uli mmusiwu. Tiyeni tikawone zotsatira za mayeso!
Results for December Summative examinations are in. Students can check with their Heads of Sections
16/05/2026
Kugona there's no.
The time table for July examinations is out, let's strive for excellence and avoid ma Sup. Good luck guy's.
15/05/2026
Breaking news: Examination results are out! We will keep you posted.
14/05/2026
Si tsiku lililonse timalowa n'class guys, limafika la Kamuzu timapuma.
12/05/2026
Amisili tonse tabwerani pano.
Boma latsekula khomo kwa mmisili wina aliyense kuti akalembetse nkukhala ndi kalata zogwilira ntchito yake mdziko muno. Khomoli alitsekula kwa mmisili yemwenso sanalowe mkalasi Kuti akaphunzire za luso. Kuti mutsate zambiri werengani kalata zili mmusizi komanso m***a kupita ku ofesi zaboma zoyeza luso la manja ku Mzuzu, Blantyre komanso ku Lilongwe ngakhale ku likulu la unduna owona za ntchito.
06/05/2026
Sankha wekha: Bwerani mudzaphunzire luso lomwe mmafuna mutakhala, kuyamba mwezi wa July ukudzawu. Ndondomeko yopanga apply ndiyomwe ija. Wonani pa flier-po.
02/05/2026
Mwayi wamaphunziro ulipo wambiri. Bwerani ku MIRACLE Technical Institute ndipo simudzakhumudwa olo pang'ono.
01/05/2026
| Monday | 08:00 - 16:00 |
| Tuesday | 08:00 - 16:00 |
| Wednesday | 08:00 - 16:00 |
| Thursday | 08:00 - 16:00 |
| Friday | 08:00 - 16:00 |
| Saturday | 07:00 - 18:00 |
| Sunday | 08:00 - 12:00 |