Mulungu amakonda aliyense amene amamuvera ndi kuchita chifuniro chake
Yesu ndi yankho
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Yesu ndi yankho, Tutor/Teacher, Box 20 mpepa Kasungu, Kasungu.
Mukhale ndi chidziwitso pakupanga zinthu
ana anu makhalidwe abwino awapatse mulungu mu dzina la Yesu Khristu mwana wa Mulungu wa moyo
Mulungu mutigonetse tulo ta bwino
Ndiyamika yehova wanga olenga kumwamwa ndi dziko olenga iweso ndi ine
Tiyeni tiwerengere limofzi pa aroma 8vs12 pomwe akuti 12Cifukwa cace, abale, ife tiri amangawa si ace a thupi ai, kukhala ndi moyo monga mwa thupi; 13pakuti ngati mukhala ndi moyo monga mwa thupi, mudzafa; koma ngati ndi mzimu mufetsa zocita zace za thupi, mudzakhala ndi moyo. 14Pakuti onse amene atsogozedwa ndi Mzimu wa Mulungu, amenewo ali ana a Mulungu, 15Pakuti inu simunalandira mzimu wa ukapolo kucitanso mantha; koma munalandira mzimu waumwana, umene tipfuula nao, kuti, Abba, Atate, 16Mzimu yekha acita umboni pamodzi ndi mzimu wathu, kuti tiri ana a Mulungu;
Mulungu wakhala thandizo ponitandiza machitidwe onse kuti nditsekure peji ili tikhala tikuphuzira mau a mulungu pano mulungu azikudalitsani ngati mwapanga like or following my page
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Box 20 Mpepa Kasungu
Kasungu