Mwana wa Neba

Mwana wa Neba

Share

Be kind be sweet be hot be humble 🍌🍎🍓

16/01/2025

miss alot of people

Photos from Mwana wa Neba's post 04/09/2024

Done everything..... thanks third construction....👍👍
Number ndiyomwe ija 0985906823

29/07/2024

Kod mwapanga Kare wiring nyumba yanu? Tiyankhulen ngat mukufuna wiring 0985906823/0881137301

Photos from Mwana wa Neba's post 27/06/2024

💪💪👌
Tiyankhulen 0985906823/0881137301

Photos from Mwana wa Neba's post 22/05/2024

Azanu zikutheka ndipo akusimba lokoma inuyo mukuti bwanj? Nyumba yanu ija magesi alowa lit?

Ndilipo ine kukupangiran
+265985906823
+265881137301
Alex Banda

18/05/2024

*Mwazuka bwanji mabwana nonse mumadera mose*

Muli ndi mwawi wogobesa nyumba yanu pamutengo wazii tiyankhulen ifeyo tikakupangiran mwaluso

Kwa nonse amene mukufuna kulowesa magesi pa program ya malepu tiyankhulen tikuthandizeni!

Kwa nonse amene mukufuna kugura ma solar panels komaso ma batteries tiyankhulen

Kwa nonse amene mukufuna kugura ma cables/nthambo tiyankhulen tikuthandizeni

Kwa nonse amene mukufuna kulipira magesi panokha zakuvutan tiyankhulen

Kwa nonse amene muli ndi nyumba mukufuna italowa magesi mwa changu tiyankhulen

Banda
+265985906823
+265881137301

01/05/2024

🚩Arsenal❤️

28/04/2024

Supporting Arsenal is the best decision I ever made

28/04/2024

Musazalozedwe kuyika ndalama ndi phone muthumba limodzi,zambiri ndifotokozabe ndikamaliza kuliraku😭😭😭😭

Photos from Mwana wa Neba's post 27/04/2024

*Good morning my client/customers*

Kwa nonse amene munatiuza Kuti months end iyi ndi nthawi yanu kapena mwawi wanu tiuzen zochita ku inbox

Nthawi yachitukuko munthu umakhara ndi zochita zambiri Koma kumbukan kuyika wiring munyumba zanu chifukwa magesi ndi dilu💪 komaso ndi chisankho Chapa Mwamba

Tilipano kukuthandizani kuyika magesi munyumba zanu mwaluso komaso mokuvesesan kulingana ndi nyengo yomwe tilimo

Ma number ndi omwe aja tiyankhulen nonse amene mukufuna kulowesa magesi kapena kulipira kumene ku escom mwawi ulipo tiyankhulen musachedwe zinthu zimakwera kwera mtengo

Ndine wanu wanu
Alex Banda
+265881137301
+265985906823

10/04/2024

💪
Kwa nonse amene mumakhara Madera akumamizi komwe magesi akufika kumene mwawi wanu wapadera ndi uwu

🚩Lipilan magesi pamtengo wa zii ndipo sayinan form ya Escom pamtengo wa K17500

🚩 Jobesan nyumba yanu pamtengo wa zii wikambika ndi ife💪

🚩 Pangan wiring nyumba mwaluso ndiposo mwa makono pamtengo wa ziiii

🚩Guran ma Solar panels, Regulator, inventors ndi ma batteries olimba komaso odalilika Kwa ife💪

🚩Guran zida Za magesi kwaife nga ndi ma pvc conduit ( pipes), cables,DB set,couplin, saddle, ni***es ndi Zina zambiri Kwa ife motchipa mtengo💪

🚩Ngat nyumba yanu muli ma fault tiyankhulen ifeyo tikakupangiren mwaulele

Tiyankhulen pa ma number amenewa
👇🏻👇🏻
+265985906823
+265881137301


Wa Zamagesi A Wa Zamagesi A EscomaMwana Wa [email protected]

Want your school to be the top-listed School/college in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Lilongwe Area 47. Com
Lilongwe