Ndi nyimbo iti ya Thoko Anaphi Katimba imakusangalasani
Bwalo la oyimba.
Do you love song
Hello gyz usiku wabwino
24/07/2022
ANTHU ambiri ndi odabwa chifukwa chakuti ma Page omwe amathamanga kupanga Post kukachitika scandal..sakupereka chidwi kweni kweni pazomwe wafotokoza Jelome
Izi zili mchomcho chifukwa brother wake wa Martse Foundation Jelome wabwera poyera ndikufotoza zina zomwe zinamuchitikira Martse asanamwalire malinga ndi Jelome Akuti akhulupilira kuti Martse anachita kuphedwa suunali Moto ngati mmene Anthu akunenera koma zinali zamatsenga
Komatu a Malawi ambiri ndiodabwa kuti zomwe afotokoza Jelome zili very sensitive koma ma Page omwe timawadziwa ndikujijilika Mikozi ndi GCK- kukachitika scandal sanalankhurepo kapena kofotokoza za video imeneyi
Ena Akuti mwina izi zili chomwechi chifukwa chakuti video ikukamba za chala chomwe chimawadyesa Prophet Shepherd Bushiri
Makosana amenewa akumadyera pa Facebook pano popanga post zobakila ma bige koma chilungamo akuchiziea... Oweruza Ndi mwini wake Mulungu ife Timangoulula...
Ndizaulula
Rest in peace Martse 🕊️🕊️
Chilungamo chaoneka okha pa za imfa ya matse
1Mwauka uli. 3 Bom dia
2 Good morning 4 mosheriwa.
Tulani pansi udido mwatikanik😂
16/07/2022
Pa 3 September 👪 Aziz & made.
16/07/2022
Mumafira nd iti ma w_twice wa.
15/07/2022
Nd nyimbo it ya afanawa imakusangalasani🎶
Ndinyimbo it ya malemu matse. Mumati mukavera kumasangalala🎶
Med ce. Plz chepesani kukula mtima'
Kod waxy k nd Eli nyuchi dolo ndindan.🎶
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the school
Website
Address
Song
Lilongwe
MUSIC