ZOLENGEDZA ZOLENGEDZA ZOLENGEDZA
πΌπΌπΌπΉπΉπΉπΌπΌπΌπΉπΉπΉπΌπΉπΌπΉπΌπΉπΌπΉπΌπΉπΌπΉπΌπΌπΌπΉπΉπΉπΉπΌ
IFE A AFTERLIFE INTERNATIONAL MINISTRIES AND CHURCH
TAFUNA KUKUDZIWITSANI KOMANSO KUKUITANANI KUMAPEMPHERO AMENE ACHITIKE KUMAPETO KWA CHAKA CHINO CHA 2024 ,NDIPO NDI MAPEMPHERO AAKURU KWAMBIRI AMENE ACHITIKE MOTERE :
MALO : LILONGWE AREA 25 PA DEMO
MASIKU : KUYAMBILA LAMULUNGU PA 29 DECEMBER 09:00 MAMAWA MPAKA MBEMBEMBE PA 1 JANUARY 2025 ,INDE LACHINAYI MAMAWA
MUTU : WHERE IS POWER AND HOLINESS OF THE FIRST CHURCH
CHICHEWA : ZILI KUTI MPHAMVU KOMANSO CHIYERO CHA MPINGO OYAMBA UJA ?
PORTUGUESE: ONDE ESTΓ O PODER E A SANTIDADE DA PRIMEIRA IGREJA
ZOCHITIKA :*
β UTHENGA OSASUKUNULA NDI OBAYA MOYO
β SELF DERIVERANCE
β UBATIZO WA PAMADZI
β UBATIZO WA MZIMU WOYERA
β KUDALITSA MABANJA
β 2025 PROPHECY
β MAYIMBIDWE
β THANKSGIVING
βPASTORS AND READERS CONFERENCE NDI ZOCHITIKA ZINA ZAMBILI
ANTHU OCHOKERA MUZIGAWO ZONSE ZA DZIKO LATHU LA MALAWI ,KU MOZAMBIQUE NGAKHALE KU ZAMBIA MULI OITANIDWA KOMANSO OLANDILIDWA KU MAPEMPHERO AMENEWA NDIPO KUFIKA KWANU KUDZAKHALA MDALITSO KWA IFE
KUMENEKU TIKAKHALA NDI ATUMIKI AMBILI KWAMBILI KOMABE ENA MWA IWO NDI AWA :
β PASTOR MARK MBAMBALUME
β PASTOR ISAAC MASOAMPHAMBE
β EVANGELIST MOREEN BANDA
β PASTOR PETER H THOMAS
β EVANGELIST BRIAN CHIBALE
β PROPHETESS MAI MANGANI
β EVANGELIST DEBORAH MBEWE
β SEER NKHOMA LAZARUS
KOMANSO OSAIWALA KAPOLO WAMNG'ONONG'ONO NDI OCHEPETSETSA NDI OSAYESEDWA KANTHU PAMASO PA MULUNGU FAVOURED SAITI
ANTHU NONSE KUFIKA KWANU NDI MDALITSO WAUKURU KOMANSO OWIRIKIZA KWAMBIRI KWA IFE !
KODI MUKUFUNA KUDZIWA ZAMBILI ? MULI OLANDILIDWA KUIMBA FONI KAPENA KUPANGA WHATSAPP PA MANAMBALA AWA :
β PASTOR ISAAC MASOAMPHAMBE PA +265 990 296 250
β TEACHER MARK MBAMBALUME PA +265 996 138 052
β MAI KACHAMBA PA +265 998 058 956
β SEER LAZARUS NKHOMA PA 0995 791 572
MAUTHENGA ONSE OKHUDZANA NDI ZOKONZEKERA ZONSE NDI MMENE ZIYENDERE TIKHALA TIKUKUPATSILANI MWATSATANETSATA
Mposa Alliance
Let's get together
ANTHU A MULUNGU NDAYESERA KUCHEDZA NDI ABALE ANZANGA KU GHANA ,KU NIGER,KU SOUTHAFRICA,KU MOZAMBIQUE KOMABE ONSE AKUTSIMIKIZA CHIMODZIMODZI KUTI ZINTHU SIZILI BWINO
FUNSO LANGA NDILONENA KUTI ,KODI MAIKO ONSEWO AMENE AKULAMULILANSO NDI MBUSA LAZARUS CHAKWERA NDI MCP ?
INEYO PAJA ZA NDALE SINDIPANGA NAO KOMA AMALAWI ANZANGA NDIKUFUNA NDIKUUZENI KUTI PALIBE CHIMENE INUYO MUNGACHITE KUSINTHA MAU A MULUNGU
PANO MULI PAKALAPAKALA KUKADULA ZOBVOTERA MWATI KUFUNA KUCHOTSA BOMA LA MCP PAMPANDO KUTI ZINTHU ZIYENDE BWINO
INU MUKULOTA NDITHU ,PALIBE CHIMENE CHINGAYENDE NGAKHALE PANG'ONO NDIPO PALIBE ZINTHU KUSINTHA
_Ezekiel 7:15-17"Kunja kuli lupanga, ndi m'katimo muli_ _mliri ndi njala; wokhala kuthenso adzafa ndi lupanga, ndi wokhala m'mudziyo njala ndi mliri zidzamutha. 16Ndipo_ _akupulumuka mwa iwo adzapulumuka, koma adzakhala kumapiri ngati njiwa za kuzigwa, onse_ _akubuula, ali yense m'mphulupulu zace. 17Manja onse adzalenda, ndi maondo onse adzaweyeseka ngati madzi_ ."
AMALAWI ANZANGA TIYENI TILAPE !
Nkhomaliro ya mau Mateyu 15:8 anthu awa andilemekeza ndi pakamwa pawo koma mitima yawo ilikutari ndi ine koma andilemekeza pacabe. Anthu ambiri amalalikira zotsutsa cimo, ayimbiri anthu samasekeleraso cimo, azisogoleri anthuso ndiye iiiii amacita kutikalipira, koma bwanji timacitaso macimo omwe ife timazuzura? Tiziwe kunena kuti titatha kuzuzura ife tizalangidwa cifukwa ndife amtumiki onyenga, bwanji lero tisiye zonyenga zonse ndikukhulupilika, Ambuye atithandize amen
TILI NDI MULUNGU MMODZI YEKHA YESU KHRISTU
ZISOMO NDI MTENDERE ZA AMBUYE WATHU YESU KHRISTU MULUNGU WAMOYO ZIKUCHULUKIRENI
NOTE:::
LAPANI
LAPANI
LAPANI
LAPANI MUSANAFE # # #
*ZIDA 21 ZOMENYERA NKHONDO ZA UZIMU*
πππππππππππππππ
2 Akorinto 10:3-7"Pakuti pakuyendayenda m'thupi, siticita nkhondo monga mwa thupi, 4(pakuti zida za nkhondo yathu siziri za thupi, koma zamphamvu mwa Mulungu zakupasula malinga); 5ndi kugwetsa matsutsano, ndi cokwezeka conse cimene cidzikweza pokana ddziwitso ca Mulungu, ndi kugonjetsa ganizo lonse ku kumvera kwa Kristu; 6ndi kukhala okonzeka Irubwezera cilango kusamvera konse, pamene kumvera kwanu kudzakwaniridwa. 7Kodi mupenyera zopenyeka pamaso? Ngati wina alimbika mwa yekha kuti ali wa Kristu, ayesere icinso mwa iye yekha, kuti monga iye ali wa Kristu, koteronso ife."
β Okondedwa! Ine ndimadabwa zedi kuona kuti dziko lapansi limakhala siliyasi kwambiri ndi nkhani ya nkhondo .Mmene tikunena pano maiko ali matangwa zedi kugura zida zankhondo zamakono kuphatikizapo ma IBMS ( Inter- continental Ballistic misiles ) .Maiko amachita Izi chifukwa amadziwa kuti adani awo amakhala siliyasi kwambiri pankhani yomenya nkhondo .
β Koma ndizomvetsa chisoni lero kuona ana a Mulungu akulephera kugura zida zomenyera nkhondo ndi mdaniyo.Okondedwa! Kodi mukudziwa kuti pamene talandira Yesu khristu kukhala mbuye ndi Mpulumutsi wamoyo timakhala kuti tayamba nkhondo yomenyana ndi mdaniyo .Oipayo amafuna kuti tikatayike ku gehena wamoto pamene Mulungu amafuna kuti tidzapite kumwamba Kwa muyaya .Chotero tiyeni tikhale siliyasi pankhondo.
β Pamau amene tawerenga pamwambapo ,Baibulo likutitsimikizira kuti ngakhale poyendayenda mthupi ,komabe zida za nkhondo yathu sizathupi ; Izi zili kuulula kuti nkhondo zathu sitimenya kuthupi ,chifukwa ziwanda si anthu ,ziwanda ndi mizimu chotero nkhondo zathu ndizauzimu
Aefeso 6:12"Cifukwa kuti kulimbana kwathu sitilimbana nao mwazi ndi thupi, komatu nao maukulu, ndi maulamuliro, ndi akucita zolimbika a dziko lapansi a mdima uno, ndi a uzimu a coipa m'zakumwamba. "
β Ngati ndinu mkhristu ndipo mukakumana ndi nkhondo mumafulumira kutukwana,kumenya ndewu,kulala mulicabe ndithu
MWASWERA BWANJI KULIKOSE ABALAWANGA MWA AMBUYE WATHU YESU KHRIST WA MOYO WA KUNAZARET .
MAU ACHILIMBIKITSO KWA KHRIST ALIYESE
AFILIPI 4 VS 4Kondwerani mwa Ambuye nthawi zonse: ndibwerezanso kutero, kondwerani. 5Kufatsa kwanu kuzindikirike ndi anthu onse. Ambuye ali pafupi. 6Musadere nkhawa konse; komatu m'zonse ndi pemphero, ndi pembedzero, pamodzi ndi ciyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.
AMBUYE AKUDALITSEN MOZONSE PANENE MUKUDALIRA PEMPHERO MU NYENGO ZANU ZONSE
SHALOM AND DIVINE GLORY
I THINK FOUNDERS OF DIFFERENT CHURCHES AND MINISTRIES HAS A SLIGHTEST CHANCES OF MAKING IT TO HEAVEN!!!not all,,but most of them ,,they take God for granted,,,they are doing a lot of evil things and no one is questioning them....if they mean stealing from donors assistance,,eeish,,you can't even ask them,,they are not reachable,they roal like lions, everyone must be quite,,only God will catch up with them one day ...and this verse Mathews 7:21 will be used on them
NDIKAONETSETSA ZOCHITIKA ZA IFE TIMATI MA FOUNDER FE,,MA BISHOP FE,,,IFEYO AMENE TIDAYAMBITSA MPINGO UJA,,,TIDAYAMBITSA UTUMIKI WAKUTI WAKUTI UJA,,mpata okalowa kumwamba ndiochepa kwambiri ,,ndikubwerezanso,,MPATA OKALOWA PAKHOMO LOPAPATIZA NDIOCHEPA KWAMBIRI KUSIYANA ndi mamembala wamba,,,,oti verse ija amati,, sionse onena Ambuye Ambuye adzalowa ufumu wakumwamba koma okhawo ochita chifuniro chake,,vesi imeneyi,akayigwiritsa ntchito kwambiri pama founder,,,ndipo ma founder adzadandaura kuti mesa ife TIDAYAMBITSA MPINGO,UTUMIKI WAKUTI WAKUTI,,anthu amadzadxa mmenemu,,,ndipo Yesu adxayankha kuti CHOKANI KWA INE INU OCHITA KUSAWERUZIKA,,,,,(mateyu 7:21)bolanikoni membala kaya mbusa ,,akati walakwitsa,amatha kumva kudzudzulidwa,,koma founder safikilika,,,omudzudzula palibe,,ndipo iye mwini amazimva kuti ndiokhoza zonse,,,,koma ukamberembere uli ndi anthu amenewa,,eeeish,,adzaweruza ndi Ambuye ndithu..ngati kuli anthu amanamiza azungu akunja kuti kuno akuchita ntchito zachifundo ,,mpaka azungu amathandizadi ndithu,ndipo Ambuye adziwadalitsa anthu amenewa amene amathandiza kudzera mwama founder wa,koma vuto ndi ma founder wa,,alibe chilungamo,,mathandizowo saoneka ayi,ndipo sungawafunsenso ayi,Sinanga asokola okha,,,ndikubwerezanso,ma founders Ali ndi mwayi ochepa kwambiri okalowa kumwamba!!!! COPIED FROM SOMEONE POST. FOLLOWING AND GOOD MORNING PEOPLE OF GOD
*KUOPSA KOSAWELENGA BIBLE,*
1( pemphero lako silimankhala ndi mphavu,
2) sungaudze ena za ubwino wa Yesu
3) Ziwanda zimakukakamira, lero kupempheledwa mawa kupempheleredwa pa vuto lomwelo,
4,) Afiti sakuopa amaziwa kuti mwaiwe mulibe mphavu ya kunswa magori,
5) ukamapemphera mkamwa mumangozaza malovu, cholinga ulsiye kupemphera koma ukamawelenga mawu , mawu aja amamasula ndi kudula mphavu yoipa pa moyo wako,
6) ukamapemphera umankhala ndi ulesi suchedwa kunena Amen chifukwa mawu mwaiwe Mulibe....
*Yoswa 1:8 Buku ili la cilamulo lisacoke pakamwa pako; koma ulingiriremo usana ndi usiku, kuti usamalire kucita monga mwa zonse zolembedwamo; popeza ukatero udzakometsa njira yako, nudzacita mwanzeru.* good NIGHT people of God
Ambuye akudalitseni..Amen
CHIMANDISANGALATSA NDI ICHI,
Tsiku lina anyamata ena anafusa ophuzila a Yesu panjira ina kuti,
TICITE CHIYANI KUTI TIPULUMUKE.
Ophuzila sadayankhe mowabisa or kukokela kwawo ai Koma kuti,
LAPANI NDIKUBATIZIDWA MUDZINA LA YESU KHRSTU.
Koma izi zacokela kuti zomafusana kuti umapemphera tsiku liti ,nanga ndikuti ,ukagoti ndimapemphera Sunday mpingo wakuti basi akukuwuza kuti cipulumutso kulibe.
anakuwuzani ndani kuti cipulumutso cili mutsiku lopemphera or dzina la Mpingo?
BAIBULO LANGA LIMANDIUZA KUTI ,CIPULUMUTSO CILI MWA YESU KHRISTU YEKHA BASI ,NDIKUYENDA MUCIYERO COONADI NDI CHILUNGAMO.
Osati kulandila tsiku ai.
,athu matagwanikatu kumasunga tsiku ,koma Mechi ili kumutu ,wivi mutavala ,milomo mutaphoda .
Simudziwa kuti kuziwonjezela ndi dama ? ,Ndipo adama wonse mphoto yawo ndi Gehena ndi nyanja ya Moto?
Dziwani kuti ,kupezeka pa Mpingo pomwe palibe chiyero ndikowopsa zedi .
Sikuti Mzimu Wa Mulungu amapezeka pamipingo yonse ai ,timacita kufunafuna motsogozedwa ndi Ambuye pomwe pakupezekela mphamvu ya Mulungu .
Tidziwe kuti ,Machilitso sicipulumutso ai ,kuciza olumala sicipulumutso ai ,ndi mphatso cabe basi .
Abale anga muzipemphera koma mtima mwanu muli Yesu Khristu osati kumavala dzina lacikhristu mulibe mwini dzina .
Osayiwala kuti ,Mulungu ndi mmodzi siatatu ai ,kucipangano cakale amadziwika kuti Yehova ndi maina ena ,pomwe cipangano chatsopano ndi Yesu Khristu, monga buku lacibvumbulutso likunena kuti ,ine ndine Alefa ndi Omega .
Amen.
UTHENGA WA KUTHA KWA NTHAWI Mateyu 24:7 pakuti mtundu umodzi wa anthu uzaukirana ndi mtundu wina ndi umfumu nd umfumu wina ndpo kuzakhala njala nd zivomelezi malo akuti akuti. Wokondedwa nthawi yatha kuposa mene tikulingalilira zizindikiro ndzimene zikuonekazi njala ndimeneyi palibe pemphero laolungama lomwe lizathesa zizindikirozi, tizalira mkani zakutha kwa nthawi zinali zoona Yesu atatisiya, zoona abale kupemphera kosekuja ndkuzimana zapaziko kunja tikapsere limodzi nd asataniki, mahule, anyanga, amene analemera pasi pano, tiyeni tilingalire mozama za mawuwa kt tikakumane nd Yesu amen
Mau m'mawa uno Masalmo 23:1 Yehova ndye m'busa wanga sindzasowa.Abale wanga pali Yehova wathu sitizazingwa kapena kusowa cocita cifukwa cakuti ndfe colengedwa cace, anatilenga mwaluso kenako tamcimwiraso, mucifundo cace watifelaso kuti inu ndi ine tipulumuke, lero taziphatika ndi uhule, juga, kulera, kuluka sisi, kuziphoda, kuvala matcheni pakhosi, tiyen tisiye zonyasazi cifukwa timakhomelaso YESU pamtanda kawiri conde!! conde!! conde!! tiyen tilape amen.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the school
Telephone
Website
Address
Liwonde