Chanasa Youth Club on Line

Chanasa Youth Club on Line

Share

To transform youths dwelling from chanasa community

28/06/2022

Kwacha wa kumagobo

22/06/2022

Malawi dziko langa

24/01/2022

mvura ya vuta kwa chanasa madzi ali ponseponse zambiri tikupasilani

16/01/2022

Kodi ma youth a kwa chanasa tilipo?
Pali nkhani yot tikambilane bwerani poyera

09/01/2022

Kodi njira iti yomwe achinyamata tingapange k*t 2022 chikhale Chaka chotipindulira?????

Which procedures should youths apply to have a 2022

02/11/2021

Many youths are likely requesting for financial help for school fees and clothing here. Let's join hands to help them

15/10/2021

Happy mother's day to all mother

15/01/2020

Leavng hs beatiful wfe Leavng hs excellnce home Leavng hs innocent clan
Leavng hs mavrious ministry
He deserve respect

29/04/2018


as we all know that today leadership is in our thies as youth xo lets pull up our soccles to achieve wat we want in life. Lets dream best tomorrow by refrain ourselves from malbehaviours which gonna reward us none, love our talents by it to others through this page.
NEVER BORN TO BE SLAVE
so let made up our mind and make good decision towards our future.
_NEVER_GIVE_UP_UNTIL_U_MADE_IT

02/09/2017


Kodi Mukuziwa?????
K*t tsogolo Labwno Lir Mmanja Mwako Wachinyamatawe?
Ndi Chiyani Wachita Pofikra Mwedz Wachisan Ndi Chitatatu Uno?
Ndkuziwa K*t Chakach Chasala Pang'ono K*tha, Koma Medzi Yasalay Ndiyambri M***a Kusitha Matebulo Amoyo Wano
NDIZITI ZOMWE MUDAZIKONZA KUTI MUCHAKACHI MUZICHITE??
KUFIKIRA LERO NDIZITI MWAKWANIRITSA???
Dziwa K*ti Nthaw Iliyonse Ndiyofunika Pamoyo Wako Tsono Usabwelere Mbuyo Kamba Kazomwe Ukukumana Nazo Koma Limba Zilimbe Poti Mulungu Ngwa Mayankho. CHOFUNIKA NDIKUZIWA ZOFOKA ZAKO NDIKUZIKONZA MOYENERA KUTI CHIKAMATHA CHAKACHI ZAMBIRI ZISITHE PAMOYO WAKO, . Pomaliza Ziwa K*ti Ngakhale Mdima Ungakule Bwanji Koma Kuwala Kudza Choncho Usamavutike Mdimavuto Omwe Ukukumana Nawo Koma Uzidandaula Nthawi Yomwe Wataya Pazaziiiiiiiiii
REMEMBER TO LIKE AND SHARE TO MORE FRIENDS FOR MORE UPDATES

IWEEEEEEEEEE
.Com_by_yamzy

07/08/2017

??
kafukufuku akusonyeza k*ti pa tsikana asanu alinse anai ak*tena pakati asanafike zaka 16 ndipo atsikana 15 pa tsikana 20 aliwonse akulowa nbanja asadafike zaka 18 ndera lathulino.
ziwani k*ti kuyakhula kwanu k*thandiza

Want your school to be the top-listed School/college in Mulanje?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Website

Address


Phalombe
Mulanje