Maxon Mwandira

Maxon Mwandira

Share

The stone builders refused become the great corner stone. am a single age 31

21/06/2026

The life of dependant.....

20/06/2026

Ife tili nga, tili nganganga ndi mpesa....

20/06/2026

Sabata lopambana......

17/06/2026

MASALIMO 50 : 10 -11

Pakuti zamoyo zonse za kuthengo ndi zanga,ndi ng'ombe za pa mapiri zikwi.
Ndidziwa mbalame zonse za m'mapiri,ndipo nyama za kuthengo zili ndi Ine.

13/06/2026

Maranatha!!!!!

13/06/2026

Zikomo Mbuye pondifikitsa tsiku lasabata, mutidalitse tonse tsiku la lero pamene tikhala tikukupembezani dziko lonse lapansi.

Tiyeni tipembeze Mulungu wathu tsikuli. Ndipo Mulungu azatimenyera nkhondo za moyo uno. Exodus 14:14

Mwina tikudwala sitingathe kupita ku church, pempherani pomwe mulipo Mulungu adziwa nkhawa zanu.

HAPPY SWEET SABBATH.

10/06/2026

Mkhale ndi tsiku lopamba

09/06/2026

Kodi timayamika pa zimene Mulungu watichitira? 1 Atesalonika 5: 18. Praising God with Pastor Chataika

08/06/2026

Muvi wachiponyeponye.....

07/06/2026

Nthawi zina sibwino kumangokhalira kuzifananidza ndi anzako, izi zimachotsa chimwemwe m'moyo, pedzani nthawi ndikuWerenga madalitso anu, Mudzaona ukulu wa Mulungu mu moyo wanu. Count your blessings!

Want your school to be the top-listed School/college in Mzimba?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Mzuzu
Mzimba