Mwagonako kuchipatala mu chakachi
Ngati ayi muyamikeni Mulunguππ
Bible study with Mr Harry
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Bible study with Mr Harry, Mzuzu.
Iyi ndi page yothandiza anthu kuvetsa Bible komaso kudziwitsa zina za Bible zomwe Ena sazidziwa komaso kuyankha fuso lililose lomwe anthu alinalo kuchoka Bible lomwe yankho lake limawavuta
Kodi chifukwa chani Yesu amaphuzitsa mu mafanizo?
TODAY'S VERSE Exodus 20:7
Usatchule dzina la Yehova Mulungu wako pacabe cifukwa Yehova sadzamuyesa iye wosacimwa, amene achula pacabe dzina lacelo.
KWABWELA FUSO
Kod Adam ndi hava adachimwa atagonana or atadya chipatso? Tik*tsutsana kuno tithandizeni ndipo mutipase ves lake
Ambiri Timalithawa fuso Ili
Kodi mumamukonda Mulungu?
Sunday worship click the linkππ
https://youtu.be/0qHk6jp4YHk?si=WzZkW8YqUZ-aRBm6
MAU OGONELA
YOHANE 3 : 16
PAKUTI MULUNGU ANAKONDA DZIKO LAPASI KOTELO ANAPATSA MWANA WAKE OBADWA YEKHA KUTI YESE WAKUKHULUPILIRA IYE ASATAIKE KOMA AKHALE NAWO MOYO OSATHA.
GOOD NIGHT β
Zinthu 5 zomwe zimapangitsa munthu kusapita chitsogolo;
1. kudzikweza
2.nsanje
3. kuiwala Mulungu kumadziva k*t zomwe uli nazo wazipeza chifukwa ndiwe wanzeru osat Mulungu
4.Kusathandiza ena koma muli ndi k*thekela
5.kusatenga mbali pa za Umulungu koma ma party, ma show , magulu , maukwati ndi pa fb za Mau a Mulungu sitipanga like or comment Koma za dziko
Tiyenela kusintha zochita zathu ngati tinamuvoneleza YESU ndi mitima yathu zitchito zathu zikhale chimodzimodzi
MULUNGU atithandize πππ
Kwa omwe Timapemphela Sunday Mau a lero anachoka pa buku lanji?
ife Yohane 1:1 to 18
πππ
TODAY'S VERSE
MASALIMO 50:15
Ndipo undiitane tsiku la sautso,ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza. ππ
Ambuye akudalitseni
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Contact the school
Telephone
Website
Address
Mzuzu