Transfers alert
Name : E. Nkhata (Ngwira)
From : Neno (Lisungwi Primary School)
To : Mwanza
Name : E. Chikopa
From : Lisungwi Primary School
To : Mkavu Primary School
Name : E. Mbalati
From : Mkavu Primary School
To : Lisungwi Primary School
Lisungwi Primary School 1918
Giving vital information to the public
23/09/2023
https://chat.whatsapp.com/Ed5X8iqjPnbHLvJt5YNbxk
FRIENDS OF LISUNGWI PRIMARY SCHOOL 1918 WhatsApp Group Invite
Liness Chinangwa adasankhidwa kuchoka pa Lisungwi Primary School kupita k Chiwale Secondary School. Adalibe kuthekera kulikonse kuti atha kupita kusukuluko kamba kakuchepekedwa kwake. Ngati tidapempha kuti amusunge kusukuluko kufikira dongosolo lopeza omuthandizira litachitika. Pakadali pano aphunzitsi a pa Lisungwi asonkherana ndalama yokwana K50 000.00. Komatu ndalamayi sikununkha kanthu coz fees yokha ndi K100 000.00. Ngati muli ndi kuthekera kothandiza munthu tiyeni titero.
Ndife a Malawi,
Kuthandizana ndi chikhalidwe chathu
Nsonkhano wa makolo mawa pa Lisungwi Primary School kuyambira 11 koloko m'mawa
Kalembera wa ana a sitandade 1 akuyamba lolemba pa 28 August mpaka pa 8 September, 2023.
Ana onse omwe analemba mayeso pa Lisungwi akhoza. 100% passrate
18/08/2023
Pangolin of the year 2023
10 selected to Lisungwi CDSS
1 selected to Chiwale
Chatsira Blessings - Lisungwi CDSS
Chatulukira Steven - Lisungwi CDSS
Mapingo Madalitso - Lisungwi CDSS
Mingesi Gabriel - Lisungwi CDSS
Kalinde Danken - Lisungwi CDSS
W***y Joseph - Lisungwi CDSS
Kaserema Joanna - Lisungwi CDSS
Kanjinga Vanessa - Lisungwi CDSS
Magwira Doris - Lisungwi CDSS
Nichorus Lester - Lisungwi CDSS
Liness Chinangwa - Chiwale Secondary School
Congratulations boys and girls
Atsikana athu a football ndi a netball afika mundime yotsiriza yapa zone ataswa Mkavu
Finals akukumana ndi Nkhande
Yeeeeeee!!!!
Bulu wanding'amba mtiti. Wanding'ambiranso zovala
RETURN MATCH RESULTS
NETBALL
Nkhombe 3 - 11 Lisungwi
Aggregate 8 - 29
Next match atsikanawa akumana ndi Mkavu
FOOTBALL
BOYS
Nkhombe 2 - 1 Lisungwi
Aggregate 5 - 1
Nkhombe ikumana ndi Mkavu ife tazisiya basi
GIRLS
Nkhombe 0 - 1 Lisungwi
Aggregate 1 - 1
Penalties Nkhombe 3 - 4 Lisungwi
Lisungwi ikumana ndi Mkavu game yawo yotsatira pomwe Nkhombe ikumana ndi Mwetang'ombe as best losers
The team is preparing for a return match.
NETBALL
✓Tidaponyera kale kwakuya. 28-5 zikufunika kukangotsirizitsa
FOOTBALL
Girls
✓ Tikutsalira ndi chigoli chimodzi. Kumenya mpira pagolo lidali vuto lathu lalikulu. Tikuyesetsa kukonza mbali imeneyo
✓ Atsikana athu adatopa mwachangu. Taikapo giya wina pamajowajowa powachotsa befu
Boys
✓ Tikutsalira ndi zigoli zitatu
✓ Tinali ndi mavuto pakati zomwe tikukonza
✓ Osewera athu adataya mipira mosewera mipira italiitali
✓ Kumenya pagolo lidali vuto Lina
Tikukhulupirira kukasintha zinthu pamasewera achibwereza ndipo ndikhumbo lathu kukapambana
At Lisungwi ground
*FOOTBALL (MEN)*
Lisungwi 0 - 3 Nkhombe
*(WOMEN)*
Lisungwi 0 - 1 Nkhombe
*NETBALL*
Lisungwi 28 - 5 Nkhombe
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the school
Telephone
Website
Address
M1
Neno
Opening Hours
| Monday | 07:00 - 14:30 |
| Tuesday | 07:00 - 14:30 |
| Wednesday | 07:00 - 14:30 |
| Thursday | 07:00 - 14:30 |
| Friday | 07:00 - 14:30 |