Mpasa Secondary School Phalombe For 4 2013 outgoing tisaiwalane

Mpasa Secondary School Phalombe  For 4 2013 outgoing tisaiwalane

Share

Gululu ndilokumbukilana wina ndi mzake amene anaphunzira pa mpas koma osata Secondary Skwana kapena

18/10/2021

Tiyamike Mulungu chifukwa chopezeka ndi moyo lero dzina lake likwezeke mwayenera ulemu

04/09/2021

Ndichiyani chimene mumakumbukira nthawi yomwe mumaphunzira pasukuluyi ndipo simuzaiwala

23/05/2021

Mr Kalumo alipo

30/11/2020

Mwaswela bwanji nonse komwe muliko?

01/10/2020

Mwawa madolo

20/08/2020

Anyamata ndi atsikana mulipo nanga mulikuti?

31/07/2020

Zingayambe kuiwalika tiyeni tikumbukilane

Want your school to be the top-listed School/college in Phalombe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Phalombe