tikupempha madu anu pomwe m, bale wathu wagona mu cell tsiku lachiwiri
Darul-Ssalafiyya Salima Senga-Bay
spread sunnah
TAWHEED
Dawah chiyambi chake ndimathero ake ndi Tawheed
Dawah ya mtumiki Madaliso ndi mtendere apite kwaiye inayamba ndi Tawheed ndipo mtumiki adat:
( يا أيها الناس قولوا: لا إله إلاّ الله، تفلحوا)
(Oh inu anthu nenani kuti: palibe Mulungu wina ompembeza mwachoonad koma Allah yekha basi, mupambana)
ndipo kumapeto kwa dawah yake anati:
(قاتل الله اليهود اتخذوا قبور أنبيائهم مساجد)
Allah anawatemberera ayuda adawachita manda aneneri awo kukhala mizikit(malo opemphereramo)
komanso zilichomcho mtumiki adali akupasana lonjezo ndi maswahaba ake pankhani ya Tawheed ndipo adali kuyakhula kwaiwo kt:
بايعوني على ألا تشركوا بالله شيئا
ndilonjezeni ine kt simuzamphatikiza Allah ndizinthu zina.
chomcho daee wina aliense ayenera kuyambira pa tawheed kuzatheraso pa tawheed pomwepo
غايتنا إحياء التوحيد والسنة وإماتة الشرك والبدعة
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Kamuzu Road
Salima