Thavte Secondary Thoxyn

Thavte Secondary Thoxyn

Share

To Discuss More About Education.

20/05/2022

Chimanga ndiye CHAKWELA kulibwino nding PETER ndi JOYCE kumunda ndikango CHILIMA ndekha MULUZI uli pakamwa uku ndik*tafuna KAMUZU ka gondolosi kwinaku ndikuyang'ana kumwamba kuopa ma BINGU amvula

03/07/2019

Ndabwera tsopano akufuna k*ti ndizimugawira mabuku okhodza za school monga xcholinga cha geoup imeneyi find me on watsapp using this number 0992482257

29/05/2019

most girls do not finish education?

24/09/2017

Kubwera kwatsopano muterm yatsopano kwandipangitsa kuleka zachibwana,nanga kod inu mwalekanso zazibwenzi ndikuyamba kulimbikira zageri?

23/09/2017

Tithandizane funso ili guyz agriculture, Ateacher brought asample of soil to a form four class.Usign 'sieve methed describe how the percentage of gravel,sand silt and clay.could be determined? wina aliyense akhoza kuyankha chifukwa za 4 zili maklas ammbuyowa.

15/09/2017

kod guyz tichikozekera bwanj chiterm tikukachiyambachi and kod ena sadakwatiwe kapena kukwatira? koma ndikhulupilira k*t aliyense term imeneyi akayiyamba mosangalara coz kukakhala kulandira ma 4m ones atsopano,wophweketsa thivwa izo ndizake coz akuphweketsa chigeri chokhwiya, tsono inu ma 4m one mukuyenera kukayambanu osamaphweketsa k*t "pa cdss ine ayi"kunalembedwa kale ndi Mulungu ndipo simungakusinnthe mwanzeru zanu bora kumangovomereza.apa cdss siopanda nzeru ayi koma mway ndiwo unavuta!!!

12/09/2017

guyz yafikanso nyengo yolandila mabonyo ndipo akubwerawa tidzawalandire motan? ndikakhala ine ndikuona ngat tidzawalandire ndimakofu kuwasangalalira kumeneko k*t tawalandira.nde anzanganu mudzawalandira motan?

13/08/2017

achinyata amzanga tiyen tidzisamalire kwambiri k*t tikakumanenso kachikena pathavite secondary.

30/06/2017

Kod Chibwez Ndi Sukulu Zingayendere Limodz?

Want your school to be the top-listed School/college in Salima?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Address


Salima